《古兰经》译解 - 契瓦语翻译 * - 译解目录


含义的翻译 段: (207) 章: 拜格勒
وَمِنَ ٱلنَّاسِ مَن يَشۡرِي نَفۡسَهُ ٱبۡتِغَآءَ مَرۡضَاتِ ٱللَّهِۚ وَٱللَّهُ رَءُوفُۢ بِٱلۡعِبَادِ
Ndipo pali wina mwa anthu amene akugulitsa mzimu wake chifukwa chofuna chiyanjo cha Allah; ndipo Allah Ngodekha kwa akapolo ake.[26]
[26] Ndimeyi idavumbulutsidwa pankhani yokhudzana ndi wophunzira wina wa Mtumiki (s.a.w) dzina lake Suhaib Al-Rumi. Iyeyu pamene anafuna kusamuka ku Makka kupita ku Madina ma Quraish anamutsekereza, ndipo adamuuza kuti ngati akufuna kusamuka asiye chuma chake chonse, kupanda kutero sangasamuke. Choncho adalolera kusiya chuma chake chonse pofuna kudzipulumutsa yekha kuti asamukire ku Madina. Allah anakondwera nayo nkhaniyi ndipo adavumbulutsa ndimeyi.
阿拉伯语经注:
 
含义的翻译 段: (207) 章: 拜格勒
章节目录 页码
 
《古兰经》译解 - 契瓦语翻译 - 译解目录

古兰经契瓦文译解,哈利德·伊布拉欣·比德拉翻译,2020年版

关闭