《古兰经》译解 - 契瓦语翻译 * - 译解目录


含义的翻译 段: (85) 章: 艾尔拉夫
وَإِلَىٰ مَدۡيَنَ أَخَاهُمۡ شُعَيۡبٗاۚ قَالَ يَٰقَوۡمِ ٱعۡبُدُواْ ٱللَّهَ مَا لَكُم مِّنۡ إِلَٰهٍ غَيۡرُهُۥۖ قَدۡ جَآءَتۡكُم بَيِّنَةٞ مِّن رَّبِّكُمۡۖ فَأَوۡفُواْ ٱلۡكَيۡلَ وَٱلۡمِيزَانَ وَلَا تَبۡخَسُواْ ٱلنَّاسَ أَشۡيَآءَهُمۡ وَلَا تُفۡسِدُواْ فِي ٱلۡأَرۡضِ بَعۡدَ إِصۡلَٰحِهَاۚ ذَٰلِكُمۡ خَيۡرٞ لَّكُمۡ إِن كُنتُم مُّؤۡمِنِينَ
Nakonso kwa anthu aku Madiyan, (tidamtumiza) m’bale wawo Shuaib. Adati: “E inu anthu Anga! Gwadirani Allah. Mulibe mulungu wina koma Iye basi. Umboni owonekera wadza kuchokera kwa Mbuye wanu. Choncho pimani miyeso (yanu ya mbale) ndi masikelo mwachilungamo. Musawachepetsere anthu zinthu zawo; ndipo musaononge pa dziko pamhuyo polikonza. Kutero ndi kwabwino kwa inu ngati muli okhulupiriradi.”
阿拉伯语经注:
 
含义的翻译 段: (85) 章: 艾尔拉夫
章节目录 页码
 
《古兰经》译解 - 契瓦语翻译 - 译解目录

古兰经契瓦文译解,哈利德·伊布拉欣·比德拉翻译,2020年版

关闭