《古兰经》译解 - 契瓦语翻译 * - 译解目录


含义的翻译 段: (89) 章: 艾尔拉夫
قَدِ ٱفۡتَرَيۡنَا عَلَى ٱللَّهِ كَذِبًا إِنۡ عُدۡنَا فِي مِلَّتِكُم بَعۡدَ إِذۡ نَجَّىٰنَا ٱللَّهُ مِنۡهَاۚ وَمَا يَكُونُ لَنَآ أَن نَّعُودَ فِيهَآ إِلَّآ أَن يَشَآءَ ٱللَّهُ رَبُّنَاۚ وَسِعَ رَبُّنَا كُلَّ شَيۡءٍ عِلۡمًاۚ عَلَى ٱللَّهِ تَوَكَّلۡنَاۚ رَبَّنَا ٱفۡتَحۡ بَيۡنَنَا وَبَيۡنَ قَوۡمِنَا بِٱلۡحَقِّ وَأَنتَ خَيۡرُ ٱلۡفَٰتِحِينَ
“Ngati titabwerera m’chipembedzo chanu pambuyo potipulumutsa Allah m’menemo, ndiye kuti tampekera Allah bodza. Sikungatheke kwa ife kubwerera m’chipembedzo chimenecho pokhapokha atafuna Allah, Mbuye wathu. Mbuye wathu Ngodziwa zonse. Ndipo kwa Allah Yekha ndiko tayadzamira. Mbuye wathu! Weruzani mwa choonadi pakati pathu ndi pakati pa anthu athu. Inu Ngabwino poweruza kuposa oweruza.”
阿拉伯语经注:
 
含义的翻译 段: (89) 章: 艾尔拉夫
章节目录 页码
 
《古兰经》译解 - 契瓦语翻译 - 译解目录

古兰经契瓦文译解,哈利德·伊布拉欣·比德拉翻译,2020年版

关闭