Audio Translations of the Noble Quran Meanings

Select a voice translation then listen to Quran recitation with translation

En - English

Kumasulira mu chiyankhulo cha Chingerezi- ndi bungwe la Rowad Translation Centre.

Latanthauziridwa ndi gulu la anthu ogwira ntchito ku bungwe lotchedwa Rowad Translation Centre mothandizana ndi bungwe loyendetsa za Dawah ku dera lotchedwa Rabwa ndi bungwe lotumikira nkhani zomasulira zinthu zokhuza za Chisilamu mu zinenero zosiyanasiyana lotchedwa kuti Association for Serving Islamic Content in Languages ndi malo apa intaneti otchedwa islamHouse.com.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

Fr - Français

Kutanthauzira mu chinenero cha French-Rashid Ma'ash

Lamasuliridwa ndi Rashid Ma'ash.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

Pt - português

Kutanthauzira mu chinenero chaku Portugal - Hilmi Nasr

Latanthauziridwa ndi Dr. Hilmi Nasr. Kenako lakonzedwa moyang'aniridwa ndi bungwe lotchedwa Rowad Translation Centre.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

Nl - Nederlands

Kutanthauzira mu chinenero chaku Netherlands- ndi bungwe la Rowad Translation Centre.

Latsindikizidwa ndi bungwe lotchedwa kuti Islamic Centre laku Netherlands. Kenako linakonzedwa moyang'aniridwa ndi bungwe la Rowad Translation Centre.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

Az - azərbaycanca

Kutanthauzira mu chinenero cha Azer - ndi Ali Khan Musayev

Latanthauziridwa ndi Ali Khan Musayev. Kenako lakonzedwa moyang'aniridwa ndi bungwe lotchedwa Rowad Translation Centre, ndipo pamaperekedwa mwai owona buku lomwe lidatanthauziridwa kumayambiliro ndi cholinga chokumva maganizo a anthu owerenga ndikukonza komanso kupititsa patsogolo ndondomeko yomasulira zinthu.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

Tl - Wikang Tagalog

Kutanthauzira mu chinenero chaku Phillipine(Tagalog)-bungwe la Rowad Translation Centre

Latanthauziridwa ndi gulu la anthu ogwira ntchito ku bungwe lotchedwa Rowad Translation Centre mothandizana ndi bungwe loyendetsa za Dawah ku dera lotchedwa Rabwa ndi bungwe lotumikira nkhani zomasulira zinthu zokhuza za Chisilamu mu zinenero zosiyanasiyana lotchedwa kuti Association for Serving Islamic Content in Languages ndi malo apa intaneti otchedwa islamHouse.com.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

Zh - 中文

Kutanthauzira mu chinenero chaku China- ndi Muhammad Sulaiman

Linamasuliridwa ndi Muhammad Makin, kuunikidwa ndi Muhammad Suleiman ndi ena mwa akatswiri a chinenero.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

Vi - Tiếng Việt

Kutanthauzira mu chinenero chaku Vietnam- ndi bungwe lotchedwa Rowad Translation Centre.

Latanthauziridwa ndi gulu la anthu ogwira ntchito ku bungwe lotchedwa Rowad Translation Centre mothandizana ndi bungwe loyendetsa za Dawah ku dera lotchedwa Rabwa ndi bungwe lotumikira nkhani zomasulira zinthu zokhuza za Chisilamu mu zinenero zosiyanasiyana lotchedwa kuti Association for Serving Islamic Content in Languages ndi malo apa intaneti otchedwa islamHouse.com.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

Fa - فارسی

Kutanthauzira mu chinenero chaku Farsi-bungwe lotchedwa Rowad Translation Centre.

Latanthauziridwa ndi gulu la anthu ogwira ntchito ku bungwe lotchedwa Rowad Translation Centre mothandizana ndi bungwe loyendetsa za Dawah ku dera lotchedwa Rabwa ndi bungwe lotumikira nkhani zomasulira zinthu zokhuza za Chisilamu mu zinenero zosiyanasiyana lotchedwa kuti Association for Serving Islamic Content in Languages ndi malo apa intaneti otchedwa islamHouse.com.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

As - অসমীয়া

Kutanthauzira mu chinenero cha Asamiya - ndi Rafiqul-Islam Habibu Al-Rahman

Latanthauziridwa ndi Rafiq Al-Islam Habib Al-Rahman.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

Si - සිංහල

Kutanthauzira mu chinenero cha Sinhala-bungwe la Rowad Translation Centre.

Latanthauziridwa ndi gulu la anthu ogwira ntchito ku bungwe lotchedwa Rowad Translation Centre mothandizana ndi bungwe loyendetsa za Dawah ku dera lotchedwa Rabwa ndi bungwe lotumikira nkhani zomasulira zinthu zokhuza za Chisilamu mu zinenero zosiyanasiyana lotchedwa kuti Association for Serving Islamic Content in Languages ndi malo apa intaneti otchedwa islamHouse.com.
The audio pronunciation of the translation was supervised by the Islamic Content Association.

So - Soomaali

Kutanthauzira mu chinenero chaku Somali- Abdul-Allah Hassan Yaqub

Linatanthauziridwa ndi Abdul-Allah Hassan Yaqub.

:
0:00 0:00